Hino do Malawi (Chichewa)

Mlungu dalitsani Malaŵi
Mumsunge m'mtendere
Gonjetsani adani onse
Njala, nthenda, nsanje
Lunzitsani mitima yathu
Kuti tisaope
Mdalitse mtsogoleri nafe
Ndi mayi Malaŵi

Malaŵi ndziko lokongola
La chonde ndi ufulu
Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri
Ndithudi tadala
Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu
N'mphatso zaulere
Nkhalango, madambo abwino
Ngwokoma Malaŵi

O ufulu tigwirizane
Kukweza Malaŵi
Ndi chikondi, khama, kumvera
Timutumikire
Pa nkhondo nkana pa mtendere
Cholinga n'chimodzi
Mayi, bambo, tidzipereke
Pokweza Malaŵi

Hino do Malawi (Chichewa) (Tradução)

Letra oficial (em Chichewa)
Deus dalitsa Malawi,
Mumsunge m'mtendere.
Mais consistente com seus Gonjetsani Onse,
Ate, Nthenda, Nsanje.
Lunzitsani destino yathu,
Tisaope Kuti.
Mdalitse Mtsogo Leri morrer,
É mayi Malawi.


Malawi ndziko lokongola,
La Monde verificar ufulu,
Aspectos da m'mapiri mphepo cheque,
Ndithudi tadala.
Zigwa, somador, nthaka, dzinthu,
N'mphatso zaulere.
Nkhalango, madambo abwino.
Ngwokoma Malawi.


O Ufulu tigwirizane,
Promover o Malawi.
É chikondi, Khama, kumvera,
Timutumikire.
Pa nkhondo como lugar Mtendere,
Cholinga n'chimodzi.
Mai, colher, tidzipereke,
Pokweza Malawi.

Composição: